IRON KINGS MALATA ku LILONGWE Timapanga komaso kugulitsa malata monga IBR, VERSATILE komaso corrugated tili ndi malata opanda color komaso a color iliyose, tiliso ndi ma Ridge, valley komaso misomali ya color ndi yokhomela matabwa pa mtengo otsika, transport ndi ulere kulikose komwe inu muli,timathaso kutumiza malata kulikose komwe inu muli ndalama mumapeleka malata anu atafika 0993242921
$12