Malo ogulitsa ali ku area 51b Lilongwe mtengo 13 million
Malowa size yake ndi 16 by 31 meters Malowa mpanda mbali zitatu zinamangidwa kunatsala ndi kutsongolo ndi kuika gate Pole lamagetsi Lili malire Ngati mukufuna kudzawona kapena kudziwa zambiri mutha kuyimba pa 0992335517/0885837201