Malo ogulitsa Pali mitengo ya bluegum 800 zonse pa ntengo wa 2.5 million Ku Tiziwane Chensomba Pofika galimoto, 100 meters kufika mu nseu wa ma minbus, Plot size 49 by 25 meters Contact 0991120144
$2