Malo ogulitsa ali ku area 50 Lilongwe mbali mwa mseu

Malowa ali ku mpanda kuli quarters ndi nyumba yosamaliza ya three bedrooms self contained design Kuchoka mu mseu wa tala kufika pa plot osatha two minutes mabwana panja mumafuna Malo ambali mwa mseu wa tala ndi amenewa Mtengo ndi 11.5 million Ngati mukufuna kudziwa zambiri mutha kuyimba pa 0992335517/0885837201

FREE

seller's name'
Name: Gash M
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 20 April, 2024

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 4
product image 1
Image 2 of 4
product image 2
Image 3 of 4
product image 3
Image 4 of 4