Nyumbayi ili ku area 49 Dubai Lilongwe ili ndi three bedrooms, sitting room, dining room, kitchen stores, bathroom ndi toilet Nyumbayi ili ndi tiled Mtengo ndi 100.000 pa mwezi Ngati mukufuna kudzawona kapena kudziwa zambiri mutha kuyimba pa 0992335517/0885837201
FREE