moni abale anzanga ndimaganiza kuti akunama akamakamba zandalama zolowa Chikwama zachangu chifukwa ndinayesaso ndi bambo wina koma palibe Chomwe chinachitika paka Anandiblocka February chaka chino ndinaona post iyi pa facebook ya sister wina inalembedwa kuti BAMBO MWEMA amathandiza anthu munjira zambiri koma amatchuka kwambiri pothandiza anthu pa More
MWK7,000