Tecno camon 18i wabwinobwino opanda mavuto uyu akugulisidwa patengo wa 165 sauzande spes yake ndi 128 gb lamu ndi 4gb batele ndi 5000mah kusinthanaso zitheka mutha kuimba kepena watsapu pa 0994717277
$135