*Shallaki/Hadjod Himalaya tablets* Ndi ma mankhwala ochokela kuzitsamba omwe akuchiza matenda ngati awa 1. Amachiza arthritis/Nyamakazi, 2. Kuchiza gout kutupa ndi kuwuma Kwa Malo olumikizana mafupa 3. Kuchiza kupweteka Kwa msana, ngati mukunva kuwawa Kwa msana mukukanika kuima kapena mukuima koma movutikila mankhwala Ake ndi amenewa 4. More
MWK16