Townace Hood yogulisa. Muli gear box . Engine parts zilipadela. Blue book palibe. Matayala ndi ma rims palibe. Munali 2cr Diesel engine. Ikugulisidwa mmene ilili. Mukamanga nokha engine. (Selling as it is) Ili ku Ntcheu. Mtengo K1.7 million kukambirana pa ground. Whatsapp 0999050091
$180 Now $170