Chimanga

Tikugulitsa chimanga pamtengo wa ma 35000 Mk. Mukatifuna tiyimbilileni osati kumatifulashaso chosecho mukufuna katundu ayi,imbani kuti timvane chikadalipo ndipo APA till ndi matumba 1500 kuno Ku Lilongwe chisapo2.imbani pa 0995063609 thawi ili hose tizakuyakhani zikomo makasitomala.

MWK35,000

seller's name'
Name: Malawi
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 12 June, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0995063609
Loading recommendations...