KIC UPRIGHT FRIDGE FOR SALE Kunja uku dzuwa ndie latseguka zatenge KIC Upright fridge iyi kuti muzimwa madzi wozizira, muzikamo zinthu zina kuti zisamaonongeke. Zatengeni katundu uyu muzitakata business ya madzi, freezes komanso thombwa. Size: 288 litres Metallic inside and out 24/7 operational 100% excellent Price; K295,000 Location; Bangwe Mvula Call/Wap 0885174521/09995174521
$295