Ngati kuli chuma chosatha ndiye ndi malo. Pezani anu lero pa mtengo wabwino 5.2 million kumvananso kulipo. Pali nyumba komanso malo oti mutha kumangapo nyumba yaikulu ya kumtima kwanu. Madzi komanso magetsi zili mkhonde. Location: chiuzila pafupi ndi manda a chatama. Ngati muli ndi galimoto izikagona pakhomo panu osati kusungitsa kwa aneba kamba kosowa nsewu. Oyikonda imbani pa 0999626854/0884152042 kuti timvane pambuyo poti mwakaonapo
$5