Malo ogulitsa ali ku area 25 C Lilongwe mtengo ndi
Malo ogulitsa pali nyumba yosamaliza ndi ma quarters awiri Kukula kwa Malo ndi 15 by 30 meters Mtengo ndi 9 million Ngati mukufuna kudzawona kapena kudziwa zambiri mutha kuyimba pa phone number yanga ndi 0992335517/0885837201