Malo ogulitsa ku Blantyre ku lunzu, tikudula 20 by 30 meters, msewu ulipo, magesi alipafupi, madzinso alipafupi, kuchoka mumsewu watala ndi 500 meters, mtengo 2. Million kwacha, numbers 0999111635 call or Whatsapp, 0888651347 call only,
FREE