Ndiguleni Malo Ali ku zomba namilongo kudusa pa school kukula, kwake 60 muli fupi 83 muli Tali ndi pofika galimoto madzi magetsi zilipo pafupi mtengo ndimayamba 3 million koma apapa ikufunika ndalama mwachangu Ali ndi 2.7 abweletse katundu oposa moyo galimoto ndalama zimatha koma Malo satha phone 0885163170/0993898951
MWK2