Malo ogulitsa ku Blantyre ku lunzu tikudula 20 by 30 meters, magesi alipafupi, madzinso alipafupi, msewu ulipo, kuchoka mumsewu watala wa m1 ndi 500 meters. Numbers +265 (0) 999111635 call or Whatsapp, +265(0) 888651347 call only.
FREE