Ndikugulitsa Sansui TV yankhongo, chobelekela mwana ndi tablet Tablet idasweka touch only ndipo kukonzetsa ndi 12 pin 8gb storage 1gb ram Camera yaboh kwambiri With keyboard Sansui TV yankhongo 54 inches chakulu kwambiri no remote Chobelekela mwana chidangogwila ntchito masiku ochepa colour pink Ndili chinsapo 2 nambala 0992881720 WhatsApp
MWK16