Malo

Tili ndi malo ogulitsa ku Nanjiri kufupi ndi kuja akumanga Catholic University komanso MUBAS Malo aakulu bwino (15 by 30 meters) oikidwa kale mseu ndi ma beacon akugulitsidwa pa mtengo wa MK2, 500,000 Ndi pabwino kumangapo ma hostel kapena nyumba yokhalamo komanso ndi pafupi ndi mseu Mukafuna kumva zambiri imbani foni pa nambala iyi: +265 992 844 631 /0886772848

$2,500,000

seller's name'
Name: Andrew A
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 10 July, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0992844631
seller phone number Phone Number: 0886772848

Product Images

product image 0
Image 1 of 2
product image 1
Image 2 of 2