khalani nawo amodzi oza phunzila nawo lunso pa live training yomwe takonza mumadela onse.. kuti muzakhale ozidalira moyo wanu onse bwelani muzaphunzire kuti muzizapha makwacha mdera lanu.. Registration fee ndi 700 Fees ndi 10,000 mukabwela muzaphunzila zinthu izi kubeka cake Kupanga cream wa cake Kumuphoda cake (decoration) Kujambula More
$750