Bweletsani makobili katundu apite uyu Lifo -11 othamanga bwino Mateyalaso a new new No oil leaking Timphavu nde tilimo, eni akefe tikukwela mosakaika ndithu Ndiyankhuleni ili kuno ku Dowa mvera trading center Bweletsani 590,000 or nearest amount Imbani 0980062002 iliso pa wap Tipange business
MWK590,000