Nyumba yosatha 10 by 6.5m Yazipinda 4 stores ndi dining Mbali mwa nseu magesi ndi madzi zili pafupi.. Palinso ka space koimika galimoto or kumanga ka Quota house Ili ku Machinjiri Finishline moyang'anizana ndi furniture factory kungopambana Finishline collage Call only 0989504751 WhatsApp or call 0889478100
MWK5,000,000