Mwayi kwa onse ofuna kuphuzira kupanga sausage(4 types) , cakes & decoration, samoosa , meatballs , etc. Malo: Blantyre (South lunzu primary, machinjiri) Date:. 3 August 2024 Registration fee: k500 Training fee : k8500 Time. :8:00 am_ 4:30pm For more information contact:0998761338 / 0888663908. Or drop your number Training fee umakalipira komweko after kuphuzira. Ndipo muzagawana zonse mwapanga patsikuli kukalawa kunyumba.
$8,500