Sausage

Timagulitsa komanso kuodetsa sausage timaperekelanso Kwa omwe muli ndi ma shop kuoda mtengo ndi 3000 kwacha yokha kugula imodzi imodzi mtengo ndi 3,500 ma sausage athu ndi 100% pure beef okomanmodabwitsa timapanga supply mulingo ulionse mungafune timaphunzitsaso kapangidwe ka sausage pa mtengo okambilana Tili ku lilongwe area 23 koma kulikose timafikitsa imbani phone or Whatsapp 0991660714 0884877977

MWK3,000

seller's name'
Name: FREE M
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 05 August, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0991660714
seller phone number Phone Number: 0884877977
Loading recommendations...