Toyota passo yogulitsa Engine ndi Gearbox zosamasula Mapepala onse alipo okwanira Penti ndi yoyamba Malo ndi Thyolo, Mulenga Mileage ndi 300kms Mtengo ndi Mk4,500.000 Oikonda ndimbireni/WhatsApp pa: 0998928847
MWK4,500,000