Malo ogulitsa komaso mindailipo kuno kuzomba ilipo kumitekete komaso ku 4mailesa ndi ku odinasi alipo amitego yosiyana siyana mukakafuna mutha kuti yimbira foni pa nambaa iyi 0993340276 ndondo meko ya kagulitsedwe idzatsatidwa bwino
FREE