Mbaula za Makono za Smart Home

Gulani mbaula za makono za Smart Home pa mtengo wa K7,500. Mbaulazi ndi zolimba komanso zoseva makala. Ziliso ndi warrant ya chaka chimodzi. Ngati muli ku Lilongwe, mukatigula timakubwereserani mwaulere pa khomo panu. Madera akutali timatumiza pa Speed Courier, Bus, CTs or Ampex. Mukazifuna tiyankhuleni pa number iyi :0997783050 Whatsapp or Call. CHIDZIWITSO Anthu aku Liwonde ndi Mangochi Boma tiyankhuleni mwachangu pa number ili mwambayi tikupangeni add pa group yathu kuti tikabwera next week muzagule nawo kwanu konko.

FREE

seller's name'
Name: MALAWI B
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 19 August, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0997783050

Product Images

product image 0
Image 1 of 4
product image 1
Image 2 of 4
product image 2
Image 3 of 4
product image 3
Image 4 of 4
Loading recommendations...