Kugawula mmunda

Tikugawula mmunda pamtengo wa ziiiiii! 1hactare(2acres) =K135,000 yokha. Sitizakufunsani ya mafuta kapena chakudya. Tipatseni ntchito tiigwire. Kugawula komanso kupopota(harrowing) Tipezeni pa 0995024150/ 0880883364. Timapita kulikonse from chitipa to nsanje, nkhotakota to mchinji.

MWK135,000

seller's name'
Name: Zondi N
seller phone number
Location: Lilongwe Area 14, Lilongwe
uploaded on
Date: 19 August, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0995024150
seller phone number Phone Number: 0880883364
Loading recommendations...