Tengani bus yolimba iyi k13 mita kukambirana kulipo. Tili ku area 38 tongole kaoneni nokha. Ikungogunika kusintha ma injectors awiri basi koma zonse zili ma paper ake alipo onse. Tikugulitsa chifukwa zinthu zatithina. Tipezeni pa whatsapp +27639614935
ZAR13