Kugula tomato mumozi wa 200 kuzela pA phone pepala litha lilibe mphavu izi zikutipitisa kulesa kugula ndikugulisa Koma ukhale ndi chizindikilo cha chilombo 666 ziko laipa kugula mandasi kuzela pA phone . M new world order anati munthu ukhale ndi digital lD bank account ndi smartphone inu tiwona zambili mubado wamakono uno
FREE
