Nyumba ziwiri zogulisa pa chinamwali Zomba Sizinatalikane ndi tsika Yoyamba ndi yazipinda zitatu dining ndi sitting rooms Self contained stores Yachiwiri ndi 3 bedrooms,sitting room Self contained koma sanalumikize septic tank anakumba anawaka Madzi magetsi zilipo Mtengo ndi 14 million poyambila Imbani 0882800033 WhatsApp:0994309896
FREE