Usiku kuwala ngati masana ndima 12V solar lights, ngati mulibe magetsi inu bola mukhale ndi battery la 12v. Ngati kunyumba magetsi aliko, ndi adapter chabe bulb loyaka mothambisali basi tu ngweee panja pose. Limodzi ndupanga k7250. Mukagula ambiri kumvana kulipotu, Ka discount di, aliyese asangalale
FREE