Ma laptop abwino amene akugulisidwa pamtengo wabwino. Ma battery olimba komanso opanda ma scratches pena paliponse. Timapelekanso warranty ya miyezi itatu mkagula laptop kwa ife. Tipezeni pa Polytechnic kuno ku Blantyre. Tilindima model komanso ma brand osiyanasiyana. Tiyankhuleni pa 0995837735/0880287483
FREE