Bwelani muzatenge Munda Mzuzu chigwere Area 15 acres paliso Dimba 4 acres Madzi samaphwa , ulimi wanthilila Chaka chonse paliso pine tree wa 3years 150 mukawonjezera wina nokha mukagula Mtengo ndi Mk 8.5 million Mseu umakafika pa munda paliso ka structure ka munthu oyang'anila malowo 0993344582/0888432065
MWK850,000,000