45 ACRES MUNDA OGURITSA MSEU WA KASIYA KUDZELA KW MSUNDWE.
Munda okwana 45 acres okuguritsidwa, kwa Msundwe, mseu, opita ku Kasiya. 900,000mk per acre. Nthaka yabwino komanso mseu wabwino kufika ku, Munda. Ofuna kulima around Lilongwe, mwai ndi omwewu. Imbani pa 0995187840 ngati mungakonde.