Not selling

Khozesan ma fridge anu kwaife ndipo simuzakhumudwa anzanu akunjoya nd service yathu Ife tikamukhozera munthu Fridge timamupasa garantee ya 3month komaso amapereka ndalama fridge ikatheka Ife sitipanga zotapa ndalama ya materials ayi timagwilisa ntchito yathu tipezeni pa wap 0998011792 / 0899676892 calls

$40

seller's name'
Name: Mphatso R
seller phone number
Location: Mzuzu
uploaded on
Date: 07 September, 2024

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0998011792
seller phone number Phone Number: 0899676892
Loading recommendations...