Ngati mukufuna malata monga IBR VERSATILE komaso corrugated wa color ndi opanda color bwelani ku factory shop yathu komwe mungapezeko malata akumtima kwanu pa mtengo okambilana , timapanga malata mu size yomwe mukufuna komaso timatumiza malata kulikose komwe inu muli ndalama mumapeleka malata anu atafika kwanu, mukagula malata ambiri transport timapeleka ya ulele kupita kulikose komwe inu muli 0993242921 Kut mumve zambiri
$12