Smelton's Furnitures ili ku Mzuzu,Junction ya area 4,mmbali mwa msewu opita ku nkhokwe/NOCMA. Timagulitsa ma Tv Stands, Coffee Tables komanso timapanga katundu osiyanasiyana wamnyumba ngati ma Kitchen Units, Wardrobes, Beds, Office desks ndi zina zomwe mungafune. Timalolanso kupereka pang'onopang'ono(Lay-buy) kwa miyezi itatu. Tiimbireni kapena Whatsapp pa 0880752132 kapena 0999772098 komanso 0992329149. Kusangalatsidwa kwanu ndi chimwemwe chathu
MWK220