IRON KINGS MALATA uku ndi komwe mungapeze malata amitundu yosiyana siyana kaya mukufuna IBR VERSATILE komaso corrugated wa color ndi opanda color,tiliso ndi Ma ridge Ma valley Misomali ya color ndi yopanda color Zosez pa mtengo okambilana timagulitsa pa mtengo wa factory Ndipo timagulitsa malata kuyambila lata limodzi ngati muli kutali tiuzeni ifeyo tidzabweletsa malata kwanu konko ndalama mumapeleka malata anu atafika kumbukilani kut mukagula malata ambiri transport ndi ulere number yathu ndi 0993242921
$12