Tili ndi chimanga chogulitsa ku Zakumba Farm ku Likuni Ku Lilongwe pa mtengo wa MK39,000.00 pa thumba la 50kgs. Chimangachi ndi cholima tokha. Mukafuna kumva zambiri muyimbe phone ku 0999 311 907 kapena 0999 964 260 muti muthandizidwe. Nenani kuti mukufina matumba angati ife tikupatsani onse
MWK39,000