Nyumba yogulitsa yosamaliza yolimba ilipo kuno ku lilongwe area 18c-senti. Nyumbayi ili nseu wa dzuka P.V.T school. Septing tank iliopo yomanga kale yokuthaitha yotsekera kalenso Ikupita pa 10.5 million. Kuchotserana pang'ono kulpo. Bwerani ndiimbireni foni pa, 0883604872/0994055573.
FREE