Ogula ma laptop for breaking around Mzuzu pali TOSHIBA satellite c660 akungokhala uyu tengani pa mtengo okambila Keyboard inapoila ma keys ena ndi ena Casing yosweka mmbali mwa base 2GB RAM 111GB storage Battery 20-30 minutes Charger Pali chabe adapter Ma USB ports imavuta Koma imayaka bwino bwino. WhatsApp/Call: 0880291881/0996692484
$55,000