Ndugulisa ka passo aka engine ili bwino kwambiri ndipo ikuyenda bwino kwambiri suspension yokha ndiyomwe ikufunika kugwila.. komaso misonkho yatha business ya chilungamo iyi ndiomboleni abale anga nanu muzikwela mzuzu luwinga
MWK33