Ngati pali penapake pomwe pali madza demio kapena Suzuki swift wa smart oti akugulitsidwa ndi mwiniwake tikumufuna. Sitikufuna kupanga deal ndi agent mu njila iliyonseyo. Only yomwe ikugulitsidwa ndi aeni ake. Lilongwe
$1