Kadakalipo, paja nkhani ndiyoti, kakupanga boilo. Blue book battery ilibe . Window screen ili ndi ma crank. Eni ake akufuna 900 ngati mkulankhulana mwina mungamvane koma 900 iwo mkulankhula kwawo akuti last price. Ili pa migowi boma la phalombe 0888692090/0995900717
FREE