Bwerani muzatenge ka Suzuki almost new,engine ndi gearbox yosagwiridwa paliponse,first paint suspension mbambande ,matayara anyuwani.kungotora kumapita basi..area 25 lilongwe 0988338325Price 5.9 koma kunvanako pang'ono kulipo.Note: galimotoyi ndi almost new mafra sanagwiridweko chilichonse chili intact
$5