Ndikufuna kugula Samsung Galaxy S8+ yomwe ili mu mkhalidwe wabwino (used like new), palibe ma crack kapena vuto lililonse. Ndili ndi MWK 200,000. Ndili ku Blantyre, Limbe ndipo ndikufuna foni yomwe ingandifikire bwino. Ngati muli nayo, chonde nditumizireni pa WhatsApp kapena nditumizireni uthenga: 0987520762 Ndikuyembekezera kuyankha kwanu. Zikomo!
200,000 MWK