Wamwayi azatenge katundu wamoyo uyuu Engine komanso giyer box szinagwidweko ikadali yonse umboni mukhala nokha mukabwela , Misonkho yonse ikadali yabwino mpaka next year Mutipeza ku area 49 Mwachidule mungokhala ngat mwangotola cozz ili bwino kwambrr See more
MWK9,800,000