Guys ndabeledwa phone tecno cammon 19 ndi laptop ya hp ya mtundu wa brown ndi zovala ndi ndalama chonde kwa amene angamuwone munthu akugulisa kapena kufrashisa andiziwise pa number iyi 0990299857 azalandila 50 pin kwa amene angagule azakayakha mulandu ku police coz a airtel akupanga search nde guys samalan ndimakhala mu Mtandile ndangosamukilamo mwakumene km andilandila ndikundibela maguys help me prs