Toyota 10e iyi 5a engine just serviced kutenga kumapita vuto ndi ma panel a ziseko ziwili koma zonse intact bluebook available manual transmission zatengeni ife tinazolowera za automatic 4 mita basi mwatenga ride makani no utsi ndili ku chilinde 0988540752 only serious business mungobwera mulize kumapita
MWK4,000,000