Wamwayi ndani apa adzatenge Toyota Camry uyu pamtengo ozizila only 3.7million kumvana kulipo paground osawoopa.engine and gearbox zili intact yasmart kunja ndimkati momwe. Manual Transmission.ndikuti osowoopa kumvana kulipo call me or wap 0994114979 Lilongwe area 25
$3,700,000